2 Chronicles 8:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamanganso Betehoroni wakumtunda ndi Betehoroni wakunsi, mizinda yamalinga yokhala ndi makoma, zitseko ndi mipiringidzo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anamanganso Betehoroni wa kumtunda, ndi Betehoroni wa kunsi, midzi ya malinga yokhala nao malinga, zitseko, ndi mipiringidzo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anamanganso Beti-Horoni Wakumtunda ndi Beti-Horoni Wakumunsi, mizinda yotetezedwa yokhala ndi makoma, zitseko ndi zitsulo zotchingira,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anamanganso Betihoroni wa kumtunda, ndi Betihoroni wa kunsi, midzi ya malinga yokhala nao malinga, zitseko, ndi mipiringidzo;