2 Chronicles 8:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma analipo anthu ena otsalira a mitundu yosiyanasiyana: Ahiti, Aamori, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi. Ameneŵa sanali Aisraele,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu onse otsala mwa Ahiti, ndi Aamori, ndi Aperizi, ndi Ahivi, ndi Ayebusi, osati Aisraele,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Panali anthu amene anatsala pakati pa mitundu ya Ahiti, Aamori, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi (anthu awa sanali Aisraeli).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu onse otsala mwa Ahiti, ndi Aamori, ndi Aperizi, ndi Ahivi, ndi Ayebusi, osati Aisrayeli,