2 Chronicles 9:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komanso anyamata a mfumu Hiramu pamodzi ndi anyamata a Solomoni amene adaabwera ndi golide wa ku Ofiri, adabweranso ndi mitengo ya mbawa ndi miyala yamtengowapatali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiponso anyamata a Huramu, ndi anyamata a Solomoni otenga golide ku Ofiri, anatenga mitengo yambawa ndi timiyala ta mtengo wapatali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Anthu a Hiramu ndi anthu a Solomoni anabweretsa golide kuchokera ku Ofiri ndipo anabweretsanso mitengo ya mʼbawa ndi miyala yokongola.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiponso anyamata a Huramu, ndi anyamata a Solomo otenga golidi ku Ofiri, anatenga mitengo yambawa ndi timiyala ta mtengo wapatali.