2 Chronicles 9:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Golide amene ankabwera kwa Solomoni pa chaka chimodzi ankakwanira makilogramu 23,000,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kulemera kwake tsono kwa golide anafika kwa Solomoni chaka chimodzi ndiko matalente mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi limodzi kudza asanu ndi limodzi a golide;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kulemera kwa golide amene Solomoni amalandira pa chaka kunali makilogalamu 23,000,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kulemera kwace tsono kwa golidi anafika kwa Solomo caka cimodzi ndiko matalente mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi limodzi kudza asanu ndi limodzi a golidi;