2 Chronicles 9:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumu idapangitsanso mpando waukulu waufumu wa minyanga yanjovu niwukuta ndi golide weniweni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mfumu inapanganso mpando wachifumu waukulu wa minyanga, naukuta ndi golide woona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mfumu inapanganso mpando waukulu waufumu wa nyanga za njovu ndipo unakutidwa ndi golide woyengeka bwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mfumu inapanganso mpando wacifumu waukuru wa minyanga, naukuta ndi golidi woona.