2 Chronicles 9:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo mafumu onse a pa dziko lapansi ankafunafuna kuti amuone Solomoni ndi kumva nzeru zake zimene Mulungu adaaika mumtima mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mafumu onse a pa dziko lapansi anafuna nkhope ya Solomoni, kudzamva nzeru zake Mulungu adazilonga m'mtima mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mafumu onse a dziko lapansi ankafunafuna kuonana ndi Solomoni kuti adzamve nzeru zimene Mulungu anayika mu mtima mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mafumu onse a pa dziko lapansi anafuna nkhope ya Solomo, kudzamva nzeru zace Mulungu adazilonga m'mtima mwace.