2 Chronicles 9:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono itaona nzeru zonse za Solomoni, nyumba imene adaamanga ija,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu yaikazi ya ku Sheba ataiona nzeru ya Solomoni, ndi nyumba adaimanga,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu yayikazi ya ku Seba itaona nzeru za Solomoni komanso nyumba yaufumu imene anamanga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu yaikazi ya ku Seba ataiona nzeru ya Solomo, ndi nyumba adaimanga,