2 Chronicles 9:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo idauza mfumu Solomoni kuti, “Zimene ndinkamva ndili kudziko la kwathu zonena za ntchito zanu ndi nzeru zanu, nzoonadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa mfumu, Inali yoona mbiri ija ndidaimva m'dziko langa, ya machitidwe anu, ndi ya nzeru zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyo inati kwa mfumu, “Mbiri imene ndinamva ndili ku dziko kwathu, ya zomwe munachita komanso nzeru zanu ndi yoona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa mfumu, Inali yoona mbiri ija ndidaimva m'dziko langa, ya macitidwe anu, ndi ya nzeru zanu.