2 Corinthians 1:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Timakulemberani zokhazokha zimene mungathe kuziŵerenga ndi kuzimvetsa bwino. Ndikhulupirira kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti sitilemba kwa inu zina, koma zimene muwerenga, kapenanso muvomereza; ndipo ndiyembekeza kuti mudzavomereza kufikira chimaliziro;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti sitikukulemberani zoti simungawerenge kapena kumvetsetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti sitilemba kwa inu zina, koma zimene muwerenga, kapenanso mubvomereza; ndipo ndiyembekeza kuti mudzabvomereza kufikira cimariziro;