2 Corinthians 1:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Popeza kuti pa zimenezi ndinali wotsimikiza ndithu, ndidaaganiza zoti ndiyambe ndafika kwanuko. Ndidaafuna kuti mulandire madalitso paŵiri:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'kulimbika kumene ndinafuna kudza kwa inu kale, kuti mukakhale nacho chisomo chachiwiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza ndinatsimikiza mtima za ichi, nʼchifukwa chake ndinafuna kuti poyamba, ndidzakuchezereni kuti mupindule pawiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'kulimbika kumene ndinafuna kudza kwa inu kale, kuti mukakhalenaco cisomo caciwiri;