2 Corinthians 10:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu oganiza zotere, adziŵe kuti palibe kusiyana pakati pa zimene timanena m'makalata pamene tili nanu kutali ndi zimene timachita tikakhala nanu pamodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Woteroyo ayese ichi kuti monga tili ife ndi mau mwa akalata, pokhala palibe ife, tili oterenso m'machitidwe pokhala tili pomwepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu oterewa ayenera kuzindikira kuti zomwe timalemba mʼmakalata tili kutali ndi zomwe tidzakhale tili komweko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wotereyo ayese ici kuti monga tiri ife ndi mau mwa akalata, pokhala palibe ife, tiri oterenso m'macitidwe pokhala tiri pomwepo.