2 Corinthians 10:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sitidabzole malire athu, monga ngati sitidakafike kwanu. Tinali oyamba ndife kukafika kwanu ndi kulalika Uthenga Wabwino wonena za Khristu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti sitinyanyampiradi tokha, monga ngati sitinafikira kwa inu; pakuti tinadza kufikira inunso, mu Uthenga Wabwino wa Khristu:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti sitikudzitama modutsa malire ngati kuti sitinafike kwa inu, popeza tinali oyamba kufika kwa inu ndi Uthenga Wabwino wa Khristu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti sitinyanyampiradi tokha, monga ngati sitinafikira kwa inu; pakuti tinadza kufikira inunso, mu Uthenga Wabwino wa Kristu: