2 Corinthians 10:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi zoona kuti ndife anthu, koma sitimenya nkhondo motsata za anthu chabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti pakuyendayenda m'thupi, sitichita nkhondo monga mwa thupi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale ife timakhala mʼdziko lapansi, sitimenya nkhondo monga mmene dziko lapansi limachitira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti pakuyendayenda m'thupi, siticita nkhondo monga mwa thupi,