2 Corinthians 10:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo inu mutakhala omvera kwenikweni, tili okonzeka kulanga aliyense amene samvera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kukhala okonzeka kubwezera chilango kusamvera konse, pamene kumvera kwanu kudzakwaniridwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ife tidzakhala okonzeka kulanga aliyense wosamvera ngati inuyo mutakhala omvera kwenikweni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kukhala okonzeka Irubwezera cilango kusamvera konse, pamene kumvera kwanu kudzakwaniridwa.