2 Corinthians 11:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikadakonda kuti mundilekerere pang'ono pa kupusa kwangaku. Tandilekereranipo ndithu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Bwenzi mutandilola pang'ono ndi chopusacho! Komanso mundilole.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikukhulupirira kuti mupirira nako pangʼono kupusa kwanga. Chonde tandipirirani!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwenzi mutandilola pang'ono ndi copusaco! Komanso mundilole.