2 Corinthians 11:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malinga ndi choona cha Khristu chimene chili mwa ine, ndikunenetsa kuti palibe munthu amene adzandiletsa kunyadira zimenezi m'madera onse a ku Akaiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Choonadi cha Khristu chili mwa ine, kuti kudzitamandira kumene sikudzaletsedwa kwa ine mu mbali za Akaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kunena moona mtima molingana ndi chilungamo cha Khristu chimene chili mwa ine, palibe amene angandiletse kudzitamandira mʼzigawo za ku Akaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Coonadi ca Kristu ciri mwa ine, kuti kudzitamandira kumene sikudzaletsedwa kwa ine mu mbali za Akaya,