2 Corinthians 11:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimene ndimati ndinena panozi si zimene Ambuye afuna kuti ndinene, koma ndikungonyada, monga momwe amachitira wopusa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chimene ndilankhula sindilankhula monga mwa Ambuye, koma monga wopanda nzeru, m'kulimbika kumene kwa kudzitamandira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kudzinyadira kwangaku, sindikuyankhula monga mmene Ambuye akufunira koma ngati chitsiru.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cimene ndilankhula sindilankhula monga mwa Ambuye, koma monga wopanda nzeru, m'kulimbika kumene kwa kudzitamandira.