2 Corinthians 11:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kasanu Ayuda adandikwapula mikwapulo 39.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Ayuda ndinalandira kasanu mikwingwirima makumi anai kuperewera umodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Andikwapulapo kasanu zikoti zija za Ayuda, makumi anayi kuchotsapo chimodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kwa Ayuda ndinalandirakasanu mikwingwirima makumi anai kuperewera umodzi.