2 Corinthians 11:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati ndiyenera kunyada, ndidzanyadira kufooka kwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati ndiyenera kudzitamandira, ndidzadzitamandira ndi za kufooka kwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati nʼkoyenera kudzitamandira, ndidzadzitamandira pa zinthu zimene zimaonetsa kufowoka kwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndiyenerakudzitamandira, 4 ndidzadzitamandira ndi za kufoka kwanga.