2 Corinthians 11:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale ndine mbuli pa luso lolankhula, koma pa nzeru ndiye ai. Zimenezi ndidakuwonetsani kaŵirikaŵiri pa zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndingakhale ndili wosaphunzira m'manenedwe, koma sinditero m'chidziwitso, koma m'zonse tachionetsa kwa inu mwa anthu onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwina ndikhoza kukhala wosaphunzitsidwa kayankhulidwe, koma ndili ndi chidziwitso. Izi tinakufotokozerani momveka bwinobwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndingakhale ndiri wosaphunzira m'manenedwe, koma sinditero m'cidziwitso, koma m'zonse tacionetsa kwa inu mwa anthu onse.