2 Corinthians 11:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakulandira zondithandiza kuchokera ku mipingo ina, ndidachita ngati kuŵalanda zao kuti ndikutumikireni inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinalanda za Mipingo ina, ndi kulandira kwa iwo kulipira kuti ndikatumikire inu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinkalanda mipingo ina pomalandira thandizo kwa iwo kuti ndikutumikireni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndinalanda za Mipingo yina, ndi kulandira kwa iwo kulipira kuti ndikatumikire inu;