2 Corinthians 12:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi kapena ndidakuchenjererani mwa aliyense amene ndidamtuma kwa inu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi wina wa iwo ndinawatuma kwa inu, ndinakuchenjererani naye kodi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndinakudyerani masuku pamutu kudzera mwa wina aliyense amene ndinamutumiza kwa inu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi wina wa iwo ndinawatuma kwa inu, ndinakucenjererani naye kodi? Ndinadandaulira Tito, ndipo ndinatuma mbaleyo naye.