2 Corinthians 12:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wotere ndidzamnyadira, koma kunena za ine ndekha, sindidzanyadira kanthu kena koma kufooka kwanga kokha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha wotereyo ndidzadzitamandira; koma chifukwa cha ine ndekha sindidzadzitamandira, koma m'zofooka zanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzatamanda za munthu ngati ameneyu, koma sindidzadzitamandira ine mwini kupatula za kufowoka kwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca wotereyo ndidzadzitamandira; koma cifukwa ca Ine ndekha sindidzadzitamandira, koma m'zofoka zanga,