2 Corinthians 13:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo mudzaona chitsimikizo chimene mukufuna chakuti Khristu amalankhula kudzera mwa ine. Iyeyu sali wofooka pa zimene amachita nanu, koma amaonetsa mphamvu zake pakati panu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
popeza mufuna chitsimikizo, cha Khristu wakulankhula mwa ine; amene safooka kwa inu, koma ali wamphamvu mwa inu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
popeza mufuna chitsimikizo chakuti Khristu akuyankhula kudzera mwa ine. Iye siwofowoka pofuna kuchita nanu koma ndi wamphamvu pakati panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
popeza mufuna citsimikizo ca Kristu wakulankhula mwa ine; amene safoka kwa inu, koma ali wamphamvu mwa inu;