2 Corinthians 2:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati wina aliyense adachita kanthu kolasa mtima, si ineyo amene adalasa mtima, koma pang'ono ponse adalasako nonsenu, kunenatu mosakulitsa nkhani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati wina wachititsa chisoni, sanachititsa chisoni ine, koma pena (kuti ndisasenzetse) inu nonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati wina wamvetsa chisoni, sanamvetse chisoni ine ndekha, koma koposa mosawonjezera wakhumudwitsa nonsenu, kunenatu mosawonjezera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati wina wacititsa cisoni, sanacititsa cisoni ine, koma pena (kuti ndisasenzetse) inu nonse.