2 Corinthians 3:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sitichita ngati Mose amene ankaphimba nkhope yake ndi nsalu, kuwopa kuti Aisraele angamapenye kutha kwake kwa kuŵala kosakhalitsa kuja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo si monga Mose, amene anaika chophimba pa nkhope yake, kuti ana a Israele asayang'anitse pa chimaliziro cha chimene chinalikuchotsedwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife sitili ngati Mose amene amaphimba nkhope yake kuopa kuti Aisraeli angaone kuti kunyezimira kwa nkhope yake kumazilala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo si monga Mose, amene anaika cophimba pa nkhope yace, kuti ana a lsrayeli asayang'anitse pa cimariziro ca cimene cinalikucotsedwa;