2 Corinthians 3:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu akudziŵa kuti tikunena zimenezi chifukwa Khristu ndiye amatipatsa kulimba mtima kotere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kulimbika kotere kwa Mulungu tili nako mwa Khristu:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kulimba mtima kumeneku tili nako pamaso pa Mulungu kudzera mwa Khristu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kulimbika kotere kwa Mulungu tiri nako mwa Kristu: