2 Corinthians 3:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati ntchito yoweruza anthu kuti alangidwe inali yaulemerero, ndiye kuti ntchito yoti anthu apezeke olungama pamaso pa Mulungu idzakhala yaulemerero koposa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ngati utumiki wa chitsutso unali wa ulemerero, makamaka utumiki wa chilungamo uchulukira muulemerero kwambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati utumiki umene umatsutsa anthu unali ndi ulemerero, nanga koposa kotani ulemerero wa utumiki wobweretsa chilungamo!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ngati utumiki wa citsutso unali wa ulemerero, makamaka utumiki wa cilungamo ucurukira muulemerero kwambiri.