2 Corinthians 4:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu mwa chifundo chake adatipatsa ntchitoyi, nchifukwa chake sititaya mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake popeza tili nao utumiki umene, monga talandira chifundo, sitifooka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho popeza mwachifundo cha Mulungu tili ndi utumiki uwu, sititaya mtima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace popeza tiri nao utumiki umene, monga talandira cifundo, sitifoka;