2 Corinthians 5:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake tsono tikubuula ndi kulakalaka kuvala nyumba yathu yakumwambayo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakutinso m'menemo tibuula, ndi kukhumbitsa kuvekedwa ndi chokhalamo chathu chochokera Kumwamba;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakali pano tibuwula, ndi kulakalaka kuvala nyumba yathu ya kumwambayo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakutinso m'menemo tibuula, ndi kukhumbitsa kubvekedwa ndi cokhalamo cathu cocokera Kumwamba;