2 Corinthians 6:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikulankhula nanu ngati ana anga. Mutibwezere zomwezo zimene ifenso tidakuchitirani inu, pakutitsekulira mtima wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kukhale chibwezero chomwechi (ndinena monga ndi ana anga) mukulitsidwe inunso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pofuna kufanana zochita ndi kuyankhula monga kwa ana anga, nanunso muzinena za kukhosi kwanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kukhale cibwezero comweci (ndinena monga ndi ana anga) mukulitsidwe inunso.