2 Corinthians 6:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakhala Atate anu, inu mudzakhala ana anga aamuna ndi aakazi, akutero Ambuye Mphambe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ndidzakhala kwa inu Atate, ndi inu mudzakhala kwa Ine ana aamuna ndi aakazi, anena Ambuye Wamphamvuyonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo “Ndidzakhala Atate anu, ndipo inu mudzakhala ana anga aamuna ndi aakazi, akutero Ambuye, Wamphamvuzonse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzakhala kwa inu Atate, Ndi inu mudzakhala kwa Ine ana amunandi akazi, anena Ambuye Wamphamvuyonse.