2 Corinthians 6:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amatiyesa osadziŵika, komabe ndife odziŵika kwambiri. Amatiyesa anthu amene alikufa, komabe onani, tili moyo. Amatiyesa olangidwa, komabe sitidaphedwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
monga osadziwika, angakhale adziwika bwino; monga alinkufa, ndipo taonani tili ndi moyo; monga olangika, ndipo osaphedwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amatiyesa osadziwika komatu ndife odziwika kwambiri. Amatiyesa wooneka ngati tikufa, koma tikupitirirabe ndi moyo, okanthidwa, koma osaphedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
monga osadziwika, angakhale adziwika bwino; monga alinkufa, ndipo taonani, tiri ndi moyo; monga olangika, ndipo osaphedwa;