2 Corinthians 8:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Poti inu muli ndi zambiri tsopano, muyenera kumathandiza osoŵa, kuti m'tsogolomo nawonso akadzakhala ndi zochuluka, azidzakuthandizani pa zosoŵa zanu. Motero padzakhala kulingana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma mwa kulingana kuchuluka kwanu kukwanire kusowa kwao nthawi ya makono ano, kutinso kuchuluka kwao kukwanire kusowa kwanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zambiri zimene muli nazo pakati panu muthandize nazo osowa, kuti nawonso akadzakhala nazo zambiri adzakuthandizeni pa zosowa zanu. Cholinga nʼkuchita mofanana,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma mwa kulingana kucuruka kwanu kukwanire kusowa kwao nthawi ya makono ano, kutinso kucuruka kwao kukwanire kusowa kwanu,