2 Corinthians 8:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Malembo akuti, “Amene adapata zambiri, sizidamchulukire, amene adapata pang'ono, sizidamchepere.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuti pakhale chilingano; monga kwalembedwa, Wosonkhetsa chambiri sichinamtsalira; ndi iye wosonkhetsa pang'ono sichinamsowa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
monga kwalembedwa kuti, “Iye amene anatola zambiri sizinamutsalireko ndipo amene anatola pangʼono sizinamuchepere.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti pakhalecilingano; monga kwalembedwa, Wosonkhetsacambiri sicinamtsalira; ndi iye wosonkhetsa pang'ono sicinamsowa.