2 Corinthians 8:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti sadangochita zimene tidampempha, koma changu chake chinali chachikulu, kotero kuti adatsimikiza yekha zobwera kwanuko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakutitu analandira kudandaulira kwathu; koma pokhala nalo khama loposa, anatulukira kunka kwa inu mwini wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Tito sanangovomera kokha pempho lathu, koma yekha anafunitsitsa kwambiri kubwera kwa inu mwa iye yekha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakutitu analandira kudandaulira kwathu; koma pokhala halo khama loposa, anaturukira kunka kwil inu mwini wace.