2 Corinthians 8:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamodzi ndi iyeyo tikutuma mbale wathu uja, amene mipingo yonse ikumuyamika chifukwa cha ntchito yake yolalika Uthenga Wabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tatuma pamodzi naye mbaleyo, amene kusimba kwake m'Uthenga Wabwino kuli m'Mipingo yonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo tikumutumiza pamodzi ndi mʼbale amene mipingo yonse yamuyamikira chifukwa cha utumiki wake wa Uthenga Wabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tatuma pamodzi naye mbaleyo, amene kusimba kwace m'Uthenga Wabwino kuli m'Mipingo yonse;