2 Corinthians 8:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo si pokhapo ai, komanso mipingo idamsankha kuti adzatiperekeze pokapereka zopereka zachifundozi. Tikukonza zimenezi kuti tichitire Ambuye ulemu, ndiponso kuti tiwonetse mtima wathu wofuna kuthandiza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo si ichi chokha, komanso anasankhika ndi Mipingo, apite limodzi ndi ife m'chisomo ichi, chimene tichitumikira ife, kwa ulemerero wa Ambuye, ndi kuonetsa chivomerezo chathu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chowonjezera china nʼchakuti anasankhidwa ndi mipingo kuti atiperekeze pamene ife tikukapereka zopereka, zimene tikuchita pofuna kupereka ulemu kwa Ambuye mwini ndi kuonetsa kufunitsitsa kwathu pothandiza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo si ici cokha, komanso anasankhika ndi Mipingo, apite limodzi ndi ife m'cisomo ici, cimene ticitumikira ife, kwa ulemerero wa Ambuye, ndi kuonetsa cibvomerezo cathu;