2 Corinthians 8:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sitikufuna kupatsa anthu chifukwa choti azitinenera zoipa pa mayendetsedwe athu a zopereka zachifundo zochulukazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kupewa ichi kuti wina angatitchule za kuchulukira kumene tikutumikira;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tikufuna kupewa kutikayikira kulikonse za mmene tikuyendetsera mphatso zochulukazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kupewa ici kuti wina angatichule za kucurukira kumene tikutumikira;