2 Corinthians 8:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono muŵatsimikizire chikondi chanu, kuti mipingo yonse ichiwone, ndi kudziŵa kuti sitikulakwa tikamakunyadirani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake muwatsimikizire iwo chitsimikizo cha chikondi chanu, ndi cha kudzitamandira kwathu pa inu pamaso pa Mipingo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anthu amenewa atsimikizireni za chikondi chanu ndipo adziwe chifukwa chimene ife timakunyadirani, kuti mipingo yonse iwone chimenechi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace muwatsimikizire iwo citsimikizo ca cikondi canu, ndi ca kudzitamandira kwathu pa inu pamaso pa Mipingo.