2 Corinthians 8:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndikuŵachitira umboni kuti adapereka monga adathera, ngakhalenso mopitirira pamenepo poyerekeza ndi chuma chao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti monga mwa mphamvu yao, ndichitapo umboni, inde koposa mphamvu yao,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motero ndikuchitira umboni kuti anapereka mmene akanathera, ndipo mwinanso kuposera mmene akathera kupereka. Anapereka mosakakamizidwa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti monga mwa mphamvu yao, ndicitapo umboni, inde koposa mphamvu yao,