2 Corinthians 9:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nkosafunikira kuti ndikulembereni za zopereka zothandizira anthu a Mulungu a ku Yudeya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakutitu za utumiki wa kwa oyera mtima sikufunika kwa ine kulembera inu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼkosafunika kuti ndikulembereni za utumiki othandiza anthu a Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakutitu za utumiki wa kwa oyera mtima sikufunika kwa ine kulembera inu;