2 John 1:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidakondwera kwambiri kuti ndidapeza ana anu ena akuyenda motsata choona, monga Atate adatilamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndakondwera kwakukulu kuti ndapeza ena a ana anu alikuyenda m'choonadi, monga tinalandira lamulo lochokera kwa Atate.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinakondwera kwambiri nditapeza ana anu ena akuyenda mʼchoonadi, monga Atate anatilamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndakondwera kwakukuru kuti ndapeza ena a ana anu alikuyenda m'coonadi, monga tinalandira lamulo locokera kwa Atate.