2 Kings 1:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onani, moto udatsika kumwamba nupsereza anzanga aja, pamodzi ndi anthu ao omwe. Chonde tipulumutseni, musatiwononge.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, watsika moto wakumwamba, nunyeketsa atsogoleri awiri oyamba aja pamodzi ndi makumi asanu ao; koma tsopano moyo wanga ukhale wa mtengo wake pamaso panu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taonani, moto unatsika kuchokera kumwamba ndi kupsereza atsogoleri awiri pamodzi ndi anthu awo onse. Koma tsopano musawononge moyo wanga!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, watsika mota wakumwamba, nunyeketsa atsogoleri awiri oyamba aja pamodzi ndi makumi asanu ao; koma tsopano moyo wanga ukhale wa mtengo wace pamaso panu.