2 Kings 1:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo mngelo wa Chauta adauza Eliya kuti, “Pita naye, usamuwope.” Tsono Eliya adanyamuka natsika limodzi ndi mkulu uja, kupita kwa mfumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mthenga wa Yehova anati kwa Eliya, Tsika naye, usamuopa. Nanyamuka iye, natsikira naye kwa mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mngelo wa Yehova anati kwa Eliya, “Pita naye, usamuope.” Choncho Eliya ananyamuka natsika naye limodzi kupita kwa mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mthenga wa Yehova anati kwa Eliya, Tsika naye, usamuopa. Nanyamuka iye, natsikira naye kwa mfumu.