2 Kings 1:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amithenga aja adabwerera kwa mfumu. Tsono mfumuyo idaŵafunsa kuti, “Chifukwa chiyani mwabwerera?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mithenga inabwerera kwa iye, nanena nayo, Mwabwerera chifukwa ninji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amithenga aja atabwerera kwa mfumu, mfumuyo inawafunsa kuti, “Chifukwa chiyani mwabwerera?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mithenga inabwerera kwa iye, nanena nayo, Mwabwerera cifukwa ninji?