2 Kings 1:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumuyo idafunsa amithengawo kuti, “Kodi munthu amene adaabwera kudzakumana nanuyo, namakuuzani zimenezi, ankaoneka bwanji?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye ananena nayo, Nanga maonekedwe ake a munthu anakwerayo kukomana nanu, nanena nanu mau awa, ndi otani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inafunsa amithengawo kuti, “Kodi munthu amene anabwera kudzakumana nanuyo ndi kukuwuzani zimenezi amaoneka bwanji?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye ananena nayo, Nanga maonekedwe ace a munthu anakwerayo kukomana nanu, nanena nanu mau awa, ndi otani?