2 Kings 10:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Yehu adanyamuka napita ku Samariya. Atafika pa malo otchedwa “Pogona abusa,”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ananyamuka, nachoka, namuka ku Samariya. Ndipo pokhala kunyumba yosengera ya abusa panjira,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yehu ananyamuka kupita ku Samariya. Atafika pa malo otchedwa Beti-Ekedi wa abusa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ananyamuka, nacoka, namuka ku Samariya, Ndipo pokhala ku nyumba yosengera ya abusa panjira,