2 Kings 10:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Yehu adasonkhanitsa anthu onse a mu mzinda wa Samariya naŵauza kuti, “Ahabu ankatumikira Baala pang'ono chabe. Koma ine Yehu ndidzamtumikira kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehu anasonkhanitsa anthu onse pamodzi, nanena nao, Ahabu anatumikira Baala pang'ono, koma Yehu adzamtumikira kwambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yehu anasonkhanitsa anthu onse pamodzi nawawuza kuti, “Ahabu ankatumikira Baala pangʼono chabe; Yehu adzamutumikira kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehu anasonkhanitsa anthu onse pamodzi, nanena nao, Ahabu anatumikira Baala pang'ono, koma Yehu adzamtumikira kwambiri.