2 Kings 10:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Inu mukusamalira zidzukulu za mbuyanu Ahabu, ndipo muli nawo magaleta, zida zankhondo ndiponso mizinda yamalinga. Nchifukwa chake tsono mukangolandira kalatayi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono akakufikani inu kalata uyu, popeza muli nao ana a mbuye wanu, muli naonso magaleta ndi akavalo, ndi mudzi walinga, ndi zida,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Inu mukangolandira kalatayi, popeza ana a mbuye wanu ali ndi inu ndiponso muli ndi magaleta ndi akavalo, mzinda wotetezedwa ndi zida zankhondo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono akakufikani inu kalata uyu, popeza muli nao ana a mbuye wanu; muli naonso magareta ndi akavalo, ndi mudzi walinga, ndi zida,